Machitidwe a Atumwi 26:26 - Buku Lopatulika26 Pakuti mfumuyo idziwa izi, kwa iye imene ndilankhula nayonso mosaopa: pakuti ndidziwadi kuti kulibe kanthu ka izi kadambisikira; pakuti ichi sichinachitike m'tseri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pakuti mfumuyo idziwa izi, kwa iye imene ndilankhula nayonso mosaopa: pakuti ndidziwadi kuti kulibe kanthu ka izi kadambisikira; pakuti ichi sichinachitika m'tseri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Mfumu Agripa akudziŵa zonsezi, nkuwona ndikulankhula pamaso pao momasuka. Ndikhulupirira kuti palibe kanthu nkamodzi komwe pa zimenezi kamene iwo sakadziŵa. Pakuti sizidachitike mobisika ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mfumu ikuzidziwa bwino zinthu izi, ndipo ndikuyankhula momasuka kwa iyo. Ine ndikukhulupirira kuti palibe kanthu nʼkamodzi komwe kamene sukukadziwa, chifukwa izi sizinachike mseri. Onani mutuwo |