Machitidwe a Atumwi 26:25 - Buku Lopatulika25 Koma Paulo anati, Ndilibe misala, Fesito womvekatu; koma nditulutsa mau a choonadi ndi odziletsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma Paulo anati, Ndilibe misala, Fesito womvekatu; koma nditulutsa mau a choonadi ndi odziletsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma Paulo adati, “Pepani, a Fesito olemekezeka, sindine wamisala ai. Zimene ndikunenazi nzoona ndi zanzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Paulo anayankha nati, “Wolemekezeka Festo, sindine wozungulira mutu. Zimene ndikunena ndi zoona ndiponso za nzeru. Onani mutuwo |