Machitidwe a Atumwi 26:21 - Buku Lopatulika21 Chifukwa cha izi Ayuda anandigwira mu Kachisi, nayesa kundipha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Chifukwa cha izi Ayuda anandigwira m'Kachisi, nayesa kundipha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chifukwa cha zimenezi Ayuda adandigwira m'Nyumba ya Mulungu nafuna kundipha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ichi nʼchifukwa chake Ayuda anandigwira mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu nafuna kundipha. Onani mutuwo |