Machitidwe a Atumwi 26:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Kwaloleka udzinenere wekha. Pamenepo Paulo, anatambasula dzanja nadzikanira: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Kwaloleka udzinenere wekha. Pamenepo Paulo, anatambasula dzanja nadzikanira: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Agripa adauza Paulo kuti, “Tikukulola kuti unene mau ako.” Tsono Paulo adatambalitsa dzanja lake nayamba kunena nkhani yake. Adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo Agripa anawuza Paulo kuti, “Takulola kuti unene mawu ako.” Paulo anatambasula dzanja lake nayamba kudziteteza kuti, Onani mutuwo |