Machitidwe a Atumwi 25:5 - Buku Lopatulika5 Chifukwa chake, ati, iwo amene akhoza mwa inu amuke nane potsikirako, ndipo ngati kuli kanthu kosayenera mwa munthuyo amnenere iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Chifukwa chake, ati, iwo amene akhoza mwa inu amuke nane potsikirako, ndipo ngati kuli kanthu kosayenera mwa munthuyo amnenere iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono atsogoleri anu apite nane pamodzi kumeneko, kuti akamneneze munthuyo ngatidi iye adachitapo cholakwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ena mwa atsogoleri anu apite nane kumeneko, kuti akafotokoze mlandu wa munthuyu, ngati anachita kanthu kalikonse kolakwika.” Onani mutuwo |