Machitidwe a Atumwi 25:4 - Buku Lopatulika4 Pamenepo Fesito anayankha, kuti Paulo asungike ku Kesareya, ndi kuti iye mwini adzapitako posachedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamenepo Fesito anayankha, kuti Paulo asungike ku Kesareya, ndi kuti iye mwini adzapitako posachedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Fesito adaŵauza kuti, “Paulo akusungidwa m'ndende ku Kesareya, ndipo ine ndipita komweko posachedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Festo anayankha kuti, “Paulo akusungidwa ku Kaisareya, ndipo ndipita kumeneko posachedwa. Onani mutuwo |