Machitidwe a Atumwi 25:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo Fesito m'mene analowa dziko lake, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo Fesito m'mene analowa dziko lake, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Fesito adayamba ntchito yoweruza m'chigawo chake, ndipo patapita masiku atatu, adapita ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita masiku atatu Festo atafika mʼdera lake, anachoka ku Kaisareya ndi kupita ku Yerusalemu. Onani mutuwo |