Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 24:6 - Buku Lopatulika

6 amenenso anayesa kuipsa Kachisi; amene tamgwira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 amenenso anayesa kuipsa Kachisi; amene tamgwira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Adaayesanso ngakhale kuipitsa Nyumba ya Mulungu yathu. Ndiye ife tidamgwira.” [“Tidafuna kumuweruza potsata Malamulo athu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Anayesera ngakhale kudetsa Nyumba ya Mulungu wathu. Ndiye ife tinamugwira.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 24:6
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Pilato anati kwa iwo, Mumtenge Iye inu, ndi kumweruza Iye monga mwa chilamulo chanu. Ayuda anati kwa iye, Tilibe ulamuliro wakupha munthu aliyense;


Pakuti mwatenga anthu awa, osakhala olanda za mu Kachisi, kapena ochitira mulungu wathu mwano.


Ndipo pakufuula iwo, ndi kutaya zovala zao, ndi kuwaza fumbi mumlengalenga,


ndipo sanandipeze mu Kachisi wotsutsana ndi munthu, kapena kuutsa khamu la anthu, kapena m'sunagoge kapena m'mzinda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa