Machitidwe a Atumwi 24:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo analamulira kenturiyo amsunge iye, koma akhale nao ufulu, ndipo asaletse anthu ake kumtumikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo analamulira kenturiyo amsunge iye, koma akhale nao ufulu, ndipo asaletse anthu ake kumtumikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono adalamula mtsogoleri wa gulu la asilikali kuti azimlonda, koma azimpatsakonso ufulu, osaletsa abwenzi ake kumamsamala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iye analamulira woyangʼanira asilikali 100 kuti alondere Paulo, koma azimupatsako ufulu ndiponso kulola abwenzi ake kuti adzimusamalira. Onani mutuwo |