Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 24:21 - Buku Lopatulika

21 koma mau awa amodzi okha, amene ndinafuula poimirira pakati pao, Kunena za kuuka kwa akufa ndiweruzidwa ndi inu lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 koma mau awa amodzi okha, amene ndinafuula poimirira pakati pao, Kunena za kuuka kwa akufa ndiweruzidwa ndi inu lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Koma cholakwa changa chingathe kukhala chokhachi chakuti, pamene ndidaaimirira pamaso pao, ndidaafuula kuti, ‘Mukundizenga mlandu ine lero chifukwa ndimakhulupirira kuti anthu akufa adzauka.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Koma cholakwa changa chingathe kukhala chokhachi chakuti, nditayima pamaso pawo ndinafuwula kuti, ‘Mukundiweruza ine lero chifukwa ndimakhulupirira kuti akufa adzauka.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 24:21
5 Mawu Ofanana  

Koma pozindikira Paulo kuti ena ndi Asaduki, ndi ena Afarisi, anafuula m'bwalomo, Amuna, abale, ine ndine Mfarisi, mwana wa Afarisi: andinenera mlandu wa chiyembekezo ndi kuuka kwa akufa.


ndi kukhala nacho chiyembekezo cha kwa Mulungu chimene iwo okhanso achilandira, kuti kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama.


Chifukwa cha ichi tsono ndinakupemphani inu mundione ndi kulankhula nane; pakuti chifukwa cha chiyembekezo cha Israele ndamangidwa ndi unyolo uwu.


ovutika mtima chifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu kuuka kwa akufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa