Machitidwe a Atumwi 24:20 - Buku Lopatulika20 Kapena iwo amene ali kunowa anene anapeza chosalungama chotani, poimirira ine pamaso pabwalo la akulu a milandu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Kapena iwo amene ali kunowa anene anapeza chosalungama chotani, poimirira ine pamaso pa bwalo la akulu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Kapena omwe ali panoŵa anene ngati adandipeza cholakwa pamene ndinali m'Bwalo lao Lalikulu lamilandu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Kapena awa amene ali panowa anene mlandu umene anapeza mwa ine, pamene ndinayima pamaso pa Bwalo lawo Lalikulu. Onani mutuwo |