Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 24:19 - Buku Lopatulika

19 koma panali Ayuda ena a ku Asiya, ndiwo mwenzi atakhala pano pamaso panu ndi kundinenera, ngati ali nako kanthu kotsutsa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 koma panali Ayuda ena a ku Asiya, ndiwo mwenzi atakhala pano pamaso panu ndi kundinenera, ngati ali nako kanthu kotsutsa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Koma kunali Ayuda ena a ku Asiya. Iwowo akadayenera kukhala pano pamaso panu kudzandineneza okha ngati ali nane nkanthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Koma pali Ayuda ena ochokera ku Asiya, amene amayenera kukhala pano pamaso panu, kundiyimba mlandu ngati ali ndi kalikonse konditsutsa ine.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 24:19
3 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mene anandidziwitsa kuti pali chiwembu cha pa munthuyu, pomwepo ndinamtumiza kwa inu; ndipo ndalamulira akumnenera akamnenere kwa inu.


anati, Ndidzamva mlandu wako, pamene akukunenera afika. Ndipo analamulira kuti amdikire iye m'nyumba ya milandu ya Herode.


Koma ndinawayankha, kuti machitidwe a Aroma satero, kupereka munthu asanayambe woneneredwayo kupenyana nao omnenera ndi kukhala napo podzikanira pa chomneneracho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa