Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 24:18 - Buku Lopatulika

18 popereka izi anandipeza woyeretsedwa mu Kachisi, wopanda khamu la anthu, kapena phokoso;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 popereka izi anandipeza woyeretsedwa m'Kachisi, wopanda khamu la anthu, kapena phokoso;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Pamene ndinkachita zimenezi, iwo adandipeza m'Nyumba ya Mulungu nditachita mwambo wakudziyeretsa. Panalibe konse khamu la anthu kapena chipolowe ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Pamene ndinkachita zimenezi, iwo anandipeza mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu nditachita mwambo wodziyeretsa. Panalibe gulu la anthu kapena kuti ndimachita za chisokonezo chilichonse.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 24:18
7 Mawu Ofanana  

Undifunsiranji Ine? Funsa iwo amene adamva chimene ndinalankhula nao; taona, amenewo adziwa chimene ndinanena Ine.


Aparti ndi Amedi, ndi Aelamu, ndi iwo akukhala mu Mesopotamiya, mu Yudeya, ndiponso mu Kapadokiya, mu Ponto, ndi mu Asiya;


amenewa uwatenge nudziyeretse nao pamodzi, nuwalipirire, kuti amete mutu; ndipo adzadziwa onse kuti zomveka za iwe nzachabe, koma kuti iwe wekhanso uyenda molunjika, nusunga chilamulo.


ndipo sanandipeze mu Kachisi wotsutsana ndi munthu, kapena kuutsa khamu la anthu, kapena m'sunagoge kapena m'mzinda.


Chifukwa cha izi Ayuda anandigwira mu Kachisi, nayesa kundipha.


Koma anauka ena a iwo ochokera m'sunagoge wa Alibertino, ndi Akirene, ndi Aaleksandriya, ndi mwa iwo a ku Silisiya ndi ku Asiya, natsutsana ndi Stefano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa