Machitidwe a Atumwi 24:11 - Buku Lopatulika11 popeza mukhoza kuzindikira kuti apita masiku khumi ndi awiri okha chikwerere ine ku Yerusalemu kukalambira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 popeza mukhoza kuzindikira kuti apita masiku khumi ndi awiri okha chikwerere ine ku Yerusalemu kukalambira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Inu nomwe mutha kupeza umboni wake, sipadapite masiku opitirira khumi ndi aŵiri chipitire changa ku Yerusalemu kukapembedza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Inu mukhoza kupeza umboni wake. Sipanapite masiku khumi ndi awiri chipitireni changa ku Yerusalemu kukapembedza. Onani mutuwo |