Machitidwe a Atumwi 23:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo chidauka chipolowe chachikulu, ndipo alembi ena a kwa Afarisi anaimirira, natsutsana, nanena, Sitipeza choipa chilichonse mwa munthuyu; ndipo nanga bwanji ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo chidauka chipolowe chachikulu, ndipo alembi ena a kwa Afarisi anaimirira, natsutsana, nanena, Sitipeza choipa chilichonse mwa munthuyu; ndipo nanga bwanji ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anthu aja adayamba kufuula kwambiri. Tsono aphunzitsi ena a Malamulo, a m'gulu la Afarisi, adaimirira nanenetsa kuti, “Sitikupeza konse cholakwa mwa munthuyu ai. Mwina nkukhala kuti mzimu kapena mngelo walankhula naye!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Panali phokoso lalikulu, ndipo aphunzitsi ena amalamulo amene anali a gulu la Afarisi anayimirira natsutsa kwambiri. Iwo anati, “Ife sitikupeza cholakwa ndi munthu uyu, chifukwa mwina ndi mzimu kapena mngelo amene wayankhula naye.” Onani mutuwo |