Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 23:8 - Buku Lopatulika

8 Pakutitu Asaduki anena kuti kulibe kuuka kwa akufa, kapena mngelo, kapena mzimu; koma Afarisi avomereza ponse pawiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Pakutitu Asaduki anena kuti kulibe kuuka kwa akufa, kapena mngelo, kapena mzimu; koma Afarisi avomereza ponse pawiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Paja Asaduki amati anthu sadzauka kwa akufa, ndiponso kuti kulibe angelo kapena mizimu. Koma Afarisi amakhulupirira zonsezi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Asaduki amati kulibe kuuka kwa akufa, kulibenso ngakhale angelo kapena mizimu, koma Afarisi amakhulupirira zonsezi.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 23:8
6 Mawu Ofanana  

Tsiku lomwelo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; namfunsa Iye,


Ndipo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, nanena,


Ndipo anadza kwa Iye Asaduki ena, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye,


Ndipo pamene adatero, kunakhala chilekano pakati pa Afarisi ndi Asaduki; ndipo osonkhanawo anagawikana.


Koma m'mene analikulankhula ndi anthu, ansembe ndi mdindo wa ku Kachisi ndi Asaduki anadzako,


Koma ngati Khristu alalikidwa kuti waukitsidwa kwa akufa, nanga ena mwa inu anena bwanji kuti kulibe kuuka kwa akufa?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa