Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 23:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo iwo akuimirirako anati, Ulalatira kodi mkulu wa ansembe wa Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo iwo akuimirirako anati, Ulalatira kodi mkulu wa ansembe wa Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Apo amene adaaimirira pafupi adauza Paulo kuti, “Bwanji ukunena zachipongwe kwa mkulu wa ansembe wa Mulungu?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Anthu amene anayimirira pafupi ndi Paulo anati, “Bwanji ukunyoza mkulu wa ansembe wa Mulungu?”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 23:4
3 Mawu Ofanana  

Odala muli inu m'mene adzanyazitsa inu, nadzazunza inu, nadzakunenerani monama zoipa zilizonse chifukwa cha Ine.


Pamenepo Paulo anati kwa iye, Mulungu adzakupanda iwe, khoma loyeretsedwa iwe; ndipo kodi ukhala iwe wakundiweruza mlandu monga mwa chilamulo, ndipo ulamulira andipande ine posanga chilamulo?


Ndipo Paulo anati, Sindinadziwe, abale, kuti ndiye mkulu wa ansembe; pakuti kwalembedwa, Usamnenera choipa mkulu wa anthu ako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa