Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 23:32 - Buku Lopatulika

32 Koma m'mawa mwake anasiya apakavalo amperekeze, nabwera kulinga;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Koma m'mawa mwake anasiya apakavalo amperekeze, nabwera kulinga;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 M'maŵa mwake iwo adabwerera ku linga la asilikali, nasiya okwera pa kavalo aja kuti apitirire ndi Paulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Mmawa mwake iwo anabwerera ku malo a asilikali nasiya okwera pa akavalo kuti apitirire ndi Paulo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 23:32
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene padauka chipolowe chachikulu, kapitao wamkulu anaopa kuti angamkadzule Paulo, ndipo analamulira asilikali atsike, namkwatule pakati pao, nadze naye kulowa naye m'linga.


Koma mwana wa mlongo wake wa Paulo anamva za chifwamba chao, ndipo anadza nalowa m'linga, namfotokozera Paulo.


Ndipo anaitana akenturiyo awiri, nati, Mukonzeretu asilikali mazana awiri, apite kufikira Kesareya, ndi apakavalo makumi asanu ndi awiri, ndi anthungo mazana awiri, achoke ora lachitatu la usiku;


Pamenepo ndipo asilikali, monga adawalamulira, anatenga Paulo, napita naye usiku ku Antipatri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa