Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 23:13 - Buku Lopatulika

13 ndipo iwo amene adachita chilumbiro ichi anali oposa makumi anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 ndipo iwo amene adachita chilumbiro ichi anali oposa makumi anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Anthu amene adaapangana za chiwembu chimenechi analipo opititira makumi anai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Anthu amene anakonza chiwembuchi analipo makumi anayi.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 23:13
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu anaitana Ahitofele Mgiloni, phungu wa Davide, kumzinda wake ndiwo Gilo, pamene iye analikupereka nsembe. Ndipo chiwembucho chinali cholimba; pakuti anthu anachulukachulukabe kwa Abisalomu.


Ndipo wina anauza Davide nati, Ahitofele ali pakati pa opangana chiwembu pamodzi ndi Abisalomu. Davide nati, Yehova, musandulize uphungu wa Ahitofele ukhale wopusa.


Adzakutulutsani m'masunagoge, koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu.


Ndipo kutacha, Ayuda anapangana chiwembu, nadzitemberera, ndi kunena kuti sadzadya kapena kumwa kanthu, kufikira atamupha Paulo;


Amenewo anadza kwa ansembe aakulu ndi akulu, nati, Tadzitemberera nalo temberero kuti sitidzalawa kanthu kufikira titamupha Paulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa