Machitidwe a Atumwi 22:18 - Buku Lopatulika18 ndipo ndinamuona Iye, nanena nane, Fulumira, tuluka msanga mu Yerusalemu; popeza sadzalandira umboni wako wakunena za Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndipo ndinamuona Iye, nanena nane, Fulumira, tuluka msanga m'Yerusalemu; popeza sadzalandira umboni wako wakunena za Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndidaona Ambuye akundiwuza kuti, ‘Fulumira, tuluka msangamsanga m'Yerusalemu muno, chifukwa anthuŵa sadzauvomera umboni wako wonena za Ine.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndinaona Ambuye akundiwuza kuti, ‘Fulumira! Tuluka mu Yerusalemu msangamsanga, chifukwa anthuwa sadzavomereza umboni wako wonena za Ine.’ ” Onani mutuwo |