Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 22:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo kunali, nditabwera ku Yerusalemu ndinalikupemphera mu Kachisi, ndinachita ngati kukomoka,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo kunali, nditabwera ku Yerusalemu ndinalikupemphera m'Kachisi, ndinachita ngati kukomoka,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 “Tsono ndidabwerera ku Yerusalemu, ndipo pamene ndinkapemphera m'Nyumba ya Mulungu, ndidachita ngati ndakomoka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 “Nditabwerera ku Yerusalemu, ndikupemphera mʼNyumba ya Mulungu, ndinachita ngati ndakomoka.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 22:17
8 Mawu Ofanana  

komatu kuyambira kwa iwo a mu Damasiko, ndi a mu Yerusalemu, ndi m'dziko lonse la Yudeya, ndi kwa amitundunso ndinalalikira kuti alape, natembenukire kwa Mulungu, ndi kuchita ntchito zoyenera kutembenuka mtima.


mu mphamvu ya zizindikiro ndi zozizwitsa, mu mphamvu ya Mzimu Woyera; kotero kuti ine kuyambira ku Yerusalemu ndi kuzungulirako kufikira ku Iliriko, ndinakwanitsa Uthenga Wabwino wa Khristu;


Pamenepo patapita zaka zitatu, ndinakwera kunka ku Yerusalemu kukazindikirana naye Kefa, ndipo ndinakhala kwa iye masiku khumi ndi asanu.


ndi umo anandizindikiritsa chinsinsicho mwa vumbulutso, monga ndinalemba kale mwachidule,


Ndinagwidwa ndi Mzimu tsiku la Ambuye, ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mau aakulu, ngati a lipenga,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa