Machitidwe a Atumwi 22:13 - Buku Lopatulika13 anadza kwa ine, ndipo poimirirapo anati kwa ine, Saulo, mbale, penyanso. Ndipo ine, ora lomweli ndinampenya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 anadza kwa ine, ndipo poimirirapo anati kwa ine, Saulo, mbale, penyanso. Ndipo ine, ora lomweli ndinampenya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Iyeyo adafika nadzaimirira pafupi nane, nkundiwuza kuti, ‘Mbale wanga Saulo, yambanso kupenya.’ Nthaŵi yomweyo ndidayambadi kupenya ndipo iyeyo ndidamuwona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye anayimirira pafupi nane nati, ‘Mʼbale Saulo, penyanso!’ Ndipo nthawi yomweyo ndinapenya ndikumuona iyeyo. Onani mutuwo |