Machitidwe a Atumwi 21:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo pamene anafika pamakwerero, kudatero kuti anamsenza asilikali chifukwa cha kulimbalimba kwa khamulo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo pamene anafika pamakwerero, kudatero kuti anamsenza asilikali chifukwa cha kulimbalimba kwa khamulo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tsono pamene adafika pa makwerero a kulingako, asilikali aja adachita kumnyamula, chifukwa chakuti anthuwo adaalusa zedi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Paulo atafika pa makwerero olowera ku malo a asilikaliwo, ananyamulidwa ndi asilikali chifukwa cha ukali wa anthuwo. Onani mutuwo |