Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 21:23 - Buku Lopatulika

23 Chifukwa chake uchite ichi tikuuza iwe; tili nao amuna anai amene anawinda;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Chifukwa chake uchite ichi tikuuza iwe; tili nao amuna anai amene anawinda;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ndiye inu, muchite zimene tikuuzeni ife. Tili ndi amuna anai pano amene adachita lumbiro kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 tsono iwe chita zimene ife tikuwuze. Tili nawo amuna anayi pano amene anachita lumbiro kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 21:23
6 Mawu Ofanana  

Ndipo chilamulo cha Mnaziri, atatha masiku a kusala kwake ndi ichi: azidza naye ku khomo la chihema chokomanako;


Pamenepo Mnaziriyo amete mutu wake wa kusala kwake pa khomo la chihema chokomanako, natenge tsitsi la pamutu wake wa kusala, naliike pamoto wokhala pansi pa nsembe yoyamika.


Paulo atakhala chikhalire masiku ambiri, anatsazika abale, nachoka pamenepo, napita m'ngalawa ku Siriya, pamodzi naye Prisila ndi Akwila; popeza anameta mutu wake mu Kenkrea; pakuti adawinda.


Nchiyani tsono? Adzamva ndithu kuti wafika.


Ndipo kwa Ayuda ndinakhala monga Myuda, kuti ndipindule Ayuda; kwa iwo omvera lamulo monga womvera lamulo, ngakhale sindinakhale ndekha womvera lamulo, kuti ndipindule iwo omvera malamulo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa