Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 21:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo atapita masiku awa tinakonza akatundu athu, ntikwera ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo atapita masiku awa tinakonza akatundu athu, ntikwera ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Masiku athu okhala kumeneko atatha, tidakonza ulendo wathu ndipo tidapita ku Yerusalemu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Pambuyo pake, ife tinakonzeka ndi kunyamuka kumapita ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 21:15
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene anakocheza pa Kesareya, anakwera naulonjera Mpingo, natsikira ku Antiokeya.


Ndipo zitatha izi, Paulo anatsimikiza mu mzimu wake, atapita pa Masedoniya ndi Akaya, kunka ku Yerusalemu, kuti, Nditamuka komweko ndiyenera kuonanso ku Roma.


Koma pamene tinamva izi tinamdandaulira ife ndi iwo a komweko, asakwere iye kunka ku Yerusalemu.


Pamenepo Fesito m'mene analowa dziko lake, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya.


Ndipo m'mene adatsotsa mwa iwo masiku asanu ndi atatu kapena khumi okha anatsikira ku Kesareya; ndipo m'mawa mwake anakhala pa mpando wachiweruziro, nalamulira kuti atenge Paulo.


Koma Fesito pofuna kuyesedwa wachisomo ndi Ayuda, anayankha kwa Paulo, nati, Kodi ufuna kukwera kunka ku Yerusalemu, ndi kuweruzidwa ndi ine pomwepo kunena za zinthu izi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa