Machitidwe a Atumwi 21:12 - Buku Lopatulika12 Koma pamene tinamva izi tinamdandaulira ife ndi iwo a komweko, asakwere iye kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma pamene tinamva izi tinamdandaulira ife ndi iwo a komweko, asakwere iye kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Titamva zimenezi, ife pamodzi ndi athu akumeneko tidampemphha Paulo kuti asapite ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Titamva zimenezi, ife pamodzi ndi anthu kumeneko tinamudandaulira Paulo kuti asapite ku Yerusalemu. Onani mutuwo |