Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 21:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo pokhalapo masiku ambiri, anatsika ku Yudeya mneneri, dzina lake Agabu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo pokhalapo masiku ambiri, anatsika ku Yudeya mneneri, dzina lake Agabu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ife tili kumeneko masiku angapo, kudabwera mneneri wina kuchokera ku Yudeya, dzina lake Agabu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Titakhala kumeneko masiku ambiri, kunabwera mneneri wina wochokera ku Yudeya dzina lake Agabu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 21:10
5 Mawu Ofanana  

Ndipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m'masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum'mawa anafika ku Yerusalemu,


Ndipo ananyamuka mmodzi wa iwo, dzina lake Agabu, nalosa mwa Mzimu, kuti padzakhala njala yaikulu padziko lonse lokhalamo anthu; ndiyo idadza masiku a Klaudio.


Pakuti Paulo adatsimikiza mtima apitirire pa Efeso, angataye nthawi mu Asiya; pakuti anafulumira, ngati kutheka, akhale ku Yerusalemu tsiku la Pentekoste.


Ndipo m'mene tinapeza ophunzira, tinakhalako masiku asanu ndi awiri; ndipo iwowa ananena ndi Paulo mwa Mzimu, kuti asakwere ku Yerusalemu.


Ndipo ife titatsiriza ulendo wathu wochokera ku Tiro, tinafika ku Ptolemaisi; ndipo m'mene tidalonjera abale, tinakhala nao tsiku limodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa