Machitidwe a Atumwi 21:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Kosi, ndi m'mawa mwake ku Rode, ndipo pochokerapo ku Patara; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Kosi, ndi m'mawa mwake ku Rode, ndipo pochokerapo ku Patara; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Titalaŵirana nawo, tidachoka kumeneko m'chombo, ndipo tidayenda molunjika kukafika ku Kosi. M'maŵa mwake tidakafika ku Rode, ndipo kuchokera kumeneko tidakafika ku Patara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Titalawirana nawo, tinachoka kumeneko mʼsitima ya pamadzi, ndipo tinayenda molunjika mpaka kufika ku Kosi. Mmawa mwake tinapita ku Rode, kuchokera kumeneko tinapita ku Patara. Onani mutuwo |