Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 20:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo munali nyali zambiri m'chipinda chapamwamba m'mene tinasonkhanamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo munali nyali zambiri m'chipinda chapamwamba m'mene tinasonkhanamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 M'chipinda cham'mwamba chimene tidaasonkhanamo munali nyale zambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Munali nyale zambiri mʼchipinda chammwamba mʼmene tinasonkhanamo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 20:8
4 Mawu Ofanana  

Pomwepo Ufumu wa Kumwamba udzafanizidwa ndi anamwali khumi, amene anatenga nyali zao, natuluka kukakomana ndi mkwati.


Ndipo iyeyo adzakuonetsani chipinda chachikulu chapamwamba, chokonzeka; mukakonzere kumeneko.


Ndipo pamene adalowa, anakwera kuchipinda chapamwamba, kumene analikukhalako; ndiwo Petro ndi Yohane ndi Yakobo ndi Andrea, Filipo ndi Tomasi, Bartolomeo ndi Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, ndi Simoni Zelote, ndi Yudasi mwana wa Yakobo.


Ndipo mnyamata dzina lake Yutiko anakhala pazenera, wogwidwa nato tulo tatikulu; ndipo pakukhala chifotokozere Paulo, ndipo pogwidwa nato tulo, anagwa posanja pachiwiri, ndipo anamtola wakufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa