Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 20:5 - Buku Lopatulika

5 Koma iwowa adatitsogolera, natilinda ku Troasi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma iwowa adatitsogolera, natilinda ku Troasi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Iwoŵa adatsogola nakatidikira ku Troasi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Anthu amenewa anatsogola ndipo anakatidikira ku Trowa.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 20:5
6 Mawu Ofanana  

ndipo pamene anapita pambali pa Misiya, anatsikira ku Troasi.


Koma pamene ndinadza ku Troasi kudzalalikira Uthenga Wabwino wa Khristu, ndipo pamene padanditsegukira kwa ine pakhomo, mwa Ambuye,


Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa