Machitidwe a Atumwi 20:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo m'mene atapitapita m'mbali zijazo, nawachenjeza, anadza ku Grisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo m'mene atapitapita m'mbali zijazo, nawachenjeza, anadza ku Grisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adayendera madera a komweko nalimbitsa mtima anthu ndi mau ambiri. Pambuyo pake adapita ku Grisi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anayendera madera a kumeneko, nalimbitsa mtima anthu, ndipo pomaliza pake anapita ku Grisi. Onani mutuwo |