Machitidwe a Atumwi 20:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo m'mene tidachokerapo, m'mawa mwake tinafika pandunji pa Kiyo; ndi m'mawa mwake tinangokocheza ku Samo, ndi m'mawa mwake tinafika ku Mileto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo m'mene tidachokerapo, m'mawa mwake tinafika pandunji pa Kiyo; ndi m'mawa mwake tinangokocheza ku Samo, ndi m'mawa mwake tinafika ku Mileto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tidachokanso kumeneko m'chombo, ndipo m'maŵa mwake tidakafika pafupi ndi Kiyo. M'maŵa mwakenso tidawolokera ku Samo, ndipo mkucha wake tidakafika ku Mileto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mmawa mwake tinachoka kumeneko pa sitima ya pamadzi ndipo tinafika pafupi ndi Kiyo. Tsiku linalo tinawolokera ku Samo, ndipo tsiku linanso tinafika ku Mileto. Onani mutuwo |