Machitidwe a Atumwi 20:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo pamene anakomana ndi ife ku Aso, tinamlandira, ndipo tinafika ku Mitilene. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo pamene anakomana ndi ife ku Aso, tinamlandira, ndipo tinafika ku Mitilene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pamene iye adakumana nafe ku Aso, adakwera nafe m'chombomo, ndipo tidakafika ku Mitilene. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pamene anakumana nafe ku Aso tinamutenga ndipo tinapita ku Mitilene. Onani mutuwo |