Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 20:13 - Buku Lopatulika

13 Koma ife tinatsogolera kunka kungalawa, ndipo tinapita ku Aso, pamenepo tinati timlandire Paulo; pakuti anatipangira chomwecho, koma anati ayenda pamtunda yekha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Koma ife tinatsogolera kunka kungalawa, ndipo tinapita ku Aso, pamenepo tinati timlandire Paulo; pakuti anatipangira chomwecho, koma anati ayenda pamtunda yekha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ife tidatsogola nkukakwera chombo kupita ku Aso, kumene tinkayembekeza kukatengako Paulo. Iye adaakonza motero, chifukwa adaafuna kudzera pa mtunda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ife tinatsogola kukakwera sitima ya pa madzi kupita ku Aso, kumene tinayembekeza kukatenga Paulo. Iye anakonza motero chifukwa amayenda wapansi.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 20:13
7 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mawa mwake anauka usikusiku, natuluka namuka kuchipululu, napemphera kumeneko.


Ndipo atalawirana nao, anachoka Iye, nalowa m'phiri kukapemphera.


Pamene anaona masomphenyawo, pomwepo tinayesa kutulukira kunka ku Masedoniya, poganizira kuti Mulungu anaitanira ife kulalikira Uthenga Wabwino kwa iwo.


Ndipo anadza naye mnyamata ali wamoyo, natonthozedwa kwakukulu.


Ndipo pamene anakomana ndi ife ku Aso, tinamlandira, ndipo tinafika ku Mitilene.


Koma iwowa adatitsogolera, natilinda ku Troasi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa