Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 20:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo m'mene adakwera, nanyema mkate, nadya, nakamba nao nthawi, kufikira kucha, anachokapo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo m'mene adakwera, nanyema mkate, nadya, nakamba nao nthawi, kufikira kucha, anachokapo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Kenaka Paulo adakweranso, nakanyema nao mkate, nkudya nao. Pambuyo pake adapitiriza kulankhula nao nthaŵi yaitali, nangochoka kutacha kale.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kenaka Paulo anakweranso, mʼchipinda muja nanyema buledi nadya. Atayankhula mpaka kucha, anachoka.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 20:11
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anali chikhalire m'chiphunzitso cha atumwi ndi m'chiyanjano, m'kunyema mkate ndi mapemphero.


Ndipo anadza naye mnyamata ali wamoyo, natonthozedwa kwakukulu.


Ndipo tsiku loyamba la sabata, posonkhana ife kunyema mkate, Paulo anawafotokozera mau, popeza anati achoke m'mawa mwake; ndipo ananena chinenere kufikira pakati pa usiku.


Ndipo mnyamata dzina lake Yutiko anakhala pazenera, wogwidwa nato tulo tatikulu; ndipo pakukhala chifotokozere Paulo, ndipo pogwidwa nato tulo, anagwa posanja pachiwiri, ndipo anamtola wakufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa