Machitidwe a Atumwi 20:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo potsikirako Paulo, anamgwera namfungatira, nati, Musachite phokoso, pakuti moyo wake ulipo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo potsikirako Paulo, anamgwera namfungatira, nati, Musachite phokoso, pakuti moyo wake ulipo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pamenepo Paulo adatsika, nadziponya pa mnyamatayo nkumufungatira nati, “Musavutike, ali moyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Paulo anatsika, nadziponya pa mnyamatayo, namukumbatira. Paulo anati, “Musadandaule, ali moyo!” Onani mutuwo |