Machitidwe a Atumwi 20:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m'mene anawachenjeza, analawirana nao, natuluka kunka ku Masedoniya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m'mene anawachenjeza, analawirana nao, natuluka kunka ku Masedoniya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Phokoso lija litatha, Paulo adaitanitsa ophunzira aja, naŵalimbitsa mtima. Ndipo atatsazikana nawo, adachoka napita ku Masedoniya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Litatha phokoso, Paulo anayitanitsa ophunzira ndipo atawalimbikitsa anawatsanzika ndipo ananyamuka kupita ku Makedoniya. Onani mutuwo |