Machitidwe a Atumwi 2:32 - Buku Lopatulika32 Yesu ameneyo, Mulungu anamuukitsa; za ichi tili mboni ife tonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Yesu ameneyo, Mulungu anamuukitsa; za ichi tili mboni ife tonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Yesu yemweyo Mulungu adamuukitsadi kwa akufa, ndipo tonsefe ndife mboni za zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Mulungu wamuukitsa Yesu ameneyu, ndipo ife ndife mboni za zimenezi. Onani mutuwo |