Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 2:28 - Buku Lopatulika

28 munandidziwitsa ine njira za moyo; mudzandidzaza ndi kukondwera pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 munandidziwitsa ine njira za moyo; mudzandidzaza ndi kukondwera pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Mudandidziŵitsa njira zopita ku moyo, ndipo mudzandidzaza ndi chimwemwe pamaso panu.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Inu munandidziwitsa ine njira zamoyo; Inu mudzandidzaza ndi chimwemwe pamaso panu.’

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 2:28
14 Mawu Ofanana  

Mudzandidziwitsa njira ya moyo, pankhope panu pali chimwemwe chokwanira; m'dzanja lanu lamanja muli zokondweretsa zomka muyaya.


Koma ine ndidzapenyerera nkhope yanu m'chilungamo, ndidzakhuta mtima ndi maonekedwe anu, pamene ndidzauka.


Anakupemphani moyo, mwampatsa iye; mwamtalikitsira masiku kunthawi za nthawi.


Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu.


Mundidziwitse njira zanu, Yehova; Mundiphunzitse mayendedwe anu.


Udziweramiranji moyo wanga iwe? Ndi kuzingwa m'kati mwanga? Yembekeza Mulungu, pakuti ndidzamyamikanso chifukwa cha chipulumutso cha nkhope yake.


onse akunka kwa iye sabweranso, safika kunjira za moyo;


Ndimayenda m'njira ya chilungamo, pakati pa mayendedwe a chiweruzo,


Yesu ananena naye, Ine ndine njira, ndi choonadi, ndi moyo. Palibe munthu adza kwa Atate, koma mwa Ine.


Pakuti simudzasiya moyo wanga ku dziko la akufa, kapena simudzapereka Woyera wanu aone chivunde,


Amuna inu, abale, kuloleka kunena poyera posaopa kwa inu za kholo lija Davide, kuti adamwalira naikidwanso, ndipo manda ake ali ndi ife kufikira lero lino.


Yesu, ameneyo, chifukwa cha chimwemwe choikidwacho pamaso pake, anapirira mtanda, nanyoza manyazi, nakhala padzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa