Machitidwe a Atumwi 2:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo ndidzapatsa zodabwitsa m'thambo la kumwamba, ndi zizindikiro padziko lapansi; mwazi, ndi moto, ndi mpweya wa utsi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo ndidzapatsa zodabwitsa m'thambo la kumwamba, ndi zizindikiro pa dziko lapansi; mwazi, ndi moto, ndi mpweya wa utsi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndidzachita zozizwitsa ku thambo lakumwamba, ndipo pansi pano zizindikiro izi: magazi, moto ndi utsi watolotolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo ndidzaonetsa zodabwitsa mlengalenga ndi zizindikiro pa dziko lapansi pano, ndizo magazi, moto ndi utsi watolotolo. Onani mutuwo |