Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 19:7 - Buku Lopatulika

7 Onsewo anali ngati amuna khumi ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Onsewo anali ngati amuna khumi ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Anthuwo onse pamodzi analipo ngati khumi ndi aŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Anthu onsewo analipo khumi ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 19:7
3 Mawu Ofanana  

Pamenepo kazembe, pakuona chochitikacho anakhulupirira, nadabwa nacho chiphunzitso cha Ambuye.


Ndipo pamene Paulo anaika manja ake pa iwo, Mzimu Woyera anadza pa iwo; ndipo analankhula ndi malilime, nanenera.


Ndipo iye analowa m'sunagoge, nanena molimba mtima, miyezi itatu, natsutsana ndi kukopa kunena za Ufumu wa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa