Machitidwe a Atumwi 19:5 - Buku Lopatulika5 Pamene anamva ichi, anabatizidwa m'dzina la Ambuye Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamene anamva ichi, anabatizidwa m'dzina la Ambuye Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Okhulupirira aja atamva zimenezi, adabatizidwa m'dzina la Ambuye Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atamva zimenezi, anabatizidwa mʼdzina la Ambuye Yesu. Onani mutuwo |