Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 19:41 - Buku Lopatulika

41 Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Atanena zimenezi, adauza anthu aja kuti azipita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Iye atatha kunena zimenezi anawuza gulu la anthulo kuti libalalike.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 19:41
6 Mawu Ofanana  

Amene atontholetsa kukuntha kwa nyanja, kukuntha kwa mafunde ake, ndi phokoso la mitundu ya anthu.


Mau a anzeru achete amveka koposa kufuula kwa wolamulira mwa zitsiru.


Pakutinso palipo potiopsa kuti adzatineneza za chipolowe chalero; popeza palibe chifukwa cha kufotokozera za chipiringu chimene.


Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m'mene anawachenjeza, analawirana nao, natuluka kunka ku Masedoniya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa