Machitidwe a Atumwi 19:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo ena anafuula kanthu kena, ena kanthu kena; pakuti msonkhanowo unasokonezeka; ndipo unyinji sunadziwe chifukwa chake cha kusonkhana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo ena anafuula kanthu kena, ena kanthu kena; pakuti msonkhanowo unasokonezeka; ndipo unyinji sunadziwa chifukwa chake cha kusonkhana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Msonkhano wonse wa anthu aja udangoti pwirikiti: ena akufuula zina, enanso zina; ambiri osadziŵa ndi chimene asonkhanira chomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Munali chisokonezo mʼbwalomo pakuti ena amafuwula zina, enanso zina. Anthu ambiri sanadziwe ngakhale chomwe anasonkhanira. Onani mutuwo |