Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 19:30 - Buku Lopatulika

30 Ndipo pamene Paulo anafuna kulowa kwa anthu, ophunzira ake sanamloleze.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo pamene Paulo anafuna kulowa kwa anthu, ophunzira ake sanamloleza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Paulo adaafuna kuloŵa pakati pa anthuwo, koma ophunzira sadamloleze.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Paulo anafuna kulowa pakati pa gulu la anthu, koma ophunzira anamuletsa.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 19:30
7 Mawu Ofanana  

Koma Abisai mwana wa Zeruya anamthandiza namkantha Mfilistiyo, namupha. Pomwepo anthu a Davide anamlumbirira iye nati, Inu simudzatuluka nafenso kunkhondo, kuti mungazime nyali ya Israele.


Ndipo akulu ena a Asiyanso, popeza anali abwenzi ake, anatumiza mau kwa iye, nampempha asadziponye kubwalo lakusewera.


Koma pamene ena anaumitsa mtima ndi kusamvera, nanenera zoipa Njirayo pamaso pa anthu, anawachokera, napatutsa ophunzira, nafotokozera masiku onse m'sukulu ya Tirano.


Koma Paulo anati, Ine ndine munthu Myuda, wa ku Tariso wa mu Silisiya, mfulu ya mzinda womveka; ndipo ndikupemphani mundilole ndilankhule ndi anthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa