Machitidwe a Atumwi 19:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo panali ana aamuna asanu ndi awiri a Skeva, Myuda, mkulu wa ansembe amene anachita ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo panali ana amuna asanu ndi awiri a Skeva, Myuda, mkulu wa ansembe amene anachita ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Amene ankachita zimenezi ndi ana aamuna asanu ndi aŵiri a Skeva, mkulu wa ansembe onse wachiyuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Amene ankachita zimenezi anali ana asanu ndi awiri a Skeva, mkulu wa ansembe wa Chiyuda. Onani mutuwo |