Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 18:20 - Buku Lopatulika

20 Pamene iwo anamfunsa iye kuti akhale nthawi ina yoenjezerapo, sanavomereze;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Pamene iwo anamfunsa iye kuti akhale nthawi ina yoenjezerapo, sanavomereza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pamene ameneŵa adampempha kuti akhale nawo nthaŵi yaitali, iye sadavomere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Iwo atapempha kuti akakhale nawo nthawi yayitali, iye anakana.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 18:20
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo anafika ku Efeso, ndipo iye analekana nao pamenepo: koma iye yekha analowa m'sunagoge, natsutsana ndi Ayuda.


koma anawatsanzika, nati, Akafuna Mulungu, ndidzabwera kwa inu; ndipo anachoka ku Efeso m'ngalawa.


Pakuti Paulo adatsimikiza mtima apitirire pa Efeso, angataye nthawi mu Asiya; pakuti anafulumira, ngati kutheka, akhale ku Yerusalemu tsiku la Pentekoste.


Koma za Apolo, mbaleyo, ndamuumiriza iye, adze kwa inu pamodzi ndi abale; ndipo sichinali chifuniro chake kuti adze tsopano, koma adzafika pamene aona nthawi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa