Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 18:13 - Buku Lopatulika

13 kuti, Uyu akopa anthu apembedze Mulungu pokana chilamulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 kuti, Uyu akopa anthu apembedze Mulungu pokana chilamulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Iwo adati, “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mwa njira zotsutsana ndi Malamulo athu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Iwo anati, “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mwanjira zotsutsana ndi malamulo athu.”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 18:13
7 Mawu Ofanana  

Ayuda anamyankha iye, Tili nacho chilamulo ife, ndipo monga mwa chilamulocho ayenera kufa, chifukwa anadziyesera Mwana wa Mulungu.


koma akakhala mafunso a mau ndi maina ndi chilamulo chanu; muyang'ane inu nokha; sindifuna kuweruza zimenezi.


Ndipo anafotokozera m'sunagoge masabata onse, nakopa Ayuda ndi Agriki.


nafuula, Amuna a Israele, tithandizeni; ameneyu ndi munthu uja anaphunzitsa onse ponsepo ponenera anthu, ndi chilamulo, ndi malo ano; ndiponso anatenga Agriki nalowa nao mu Kachisi, nadetsa malo ano oyera.


koma Paulo podzikanira ananena, Sindinachimwe kanthu kapena pachilamulo cha Chiyuda, kapena pa Kachisi, kapena pa Kaisara.


naimika mboni zonama, zakunena, Munthu ameneyo saleka kunenera malo oyera amene, ndi chilamulo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa