Machitidwe a Atumwi 17:7 - Buku Lopatulika7 amene Yasoni walandira; ndipo onsewo achita zokana malamulo a Kaisara; nanena kuti pali mfumu ina, Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 amene Yasoni walandira; ndipo onsewo achita zokana malamulo a Kaisara; nanena kuti pali mfumu ina, Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 ndipo Yasoni waŵalandira. Onseŵa akuchita zosagwirizana ndi malamulo a Mfumu ya ku Roma, pakunena kuti ati kulinso mfumu ina, dzina lake Yesu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yasoni ndiye anawalandira mʼnyumba mwake. Onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo a Kaisara pomanena kuti palinso mfumu ina, yotchedwa Yesu.” Onani mutuwo |