Machitidwe a Atumwi 17:27 - Buku Lopatulika27 kuti afunefune Mulungu, kapena akamfufuze ndi kumpeza, ngakhale sakhala patali ndi yense wa ife; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 kuti afunefune Mulungu, kapena akamfufuze ndi kumpeza, ngakhale sakhala patali ndi yense wa ife; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mulungu adafuna kuti anthu amufunefune, ndipo kuti pomfufuzafufuza, mwina nkumupeza. Komabe Iye sali kutali ndi aliyense mwa ife. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mulungu anachita izi kuti anthu amufunefune, ndikuti pomufunafunapo amupeze ngakhale kuti Iye sali kutali ndi aliyense wa ife. Onani mutuwo |